DRIEMO - COMPENSATION (OFFICIAL MUSIC VIDEO )
Intro Kuti mwina compensation Driemo Ndidzapereke moyo wanga Verse1 Oh mtima uwupereke, kwaine ndiwutenge Don't you worry about safety Ndidzachengetera chengetera chengetera I know mtima unaswekapo You've been there unalirapo, ululu mumtima kufikapo Ukaganizira ganizira ganizira Paiwe ndilola ndipepere, chikondi chisaperewere Olo pa ground paterere I will love you the same baby Hook Oh udzandifunse Ndikadzakuswera mtima udzandifunse Kuti mwina compensation Ndidzapereke moyo wanga x2 Verse2 Don't be scared to love me more Zakale zapita it's me and you Undiuze pomwe Pali mantha ako I know mtima umakana ukandiunika Umaona ngati Aja anakunamiza koma I wanna be your soldier Your fighter Protector Defender I just wanna be your friend for life Hook Oh udzandifunse Ndikadzakuswera mtima udzandifunse Kuti mwina compensation Ndidzapereke moyo wanga x2 Bridge Ooh udzandifunse Udzandifunse, mwina compensation ndidzapereke moyo wanga eeee Hook Oh udzandifunse Ndikadzakuswera mtima udzandifunse Kuti mwina compensation Ndidzapereke moyo wanga x2
वर्ष
2022
अवधि
3m
IMDb
7.5
Poster Feed
कलाकार
Dremo
Singer
कलाकार
Dremo
Singer
